1 Akorinto 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Thupi ndi limodzi, koma lili ndi ziwalo zambiri ndipo ziwalo zonse za thupi, ngakhale kuti nʼzambiri, zimapanga thupi limodzi.+ Ndi mmenenso zilili ndi Khristu. Agalatiya 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi+ chifukwa nonsenu ndinu amodzi mwa Khristu Yesu.+
12 Thupi ndi limodzi, koma lili ndi ziwalo zambiri ndipo ziwalo zonse za thupi, ngakhale kuti nʼzambiri, zimapanga thupi limodzi.+ Ndi mmenenso zilili ndi Khristu.
28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi+ chifukwa nonsenu ndinu amodzi mwa Khristu Yesu.+