Aefeso 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi imene ija, Khristu simunkamudziwa, munali otalikirana ndi mtundu wa Isiraeli komanso simunali nawo mʼmapangano a lonjezo.+ Munalibe chiyembekezo ndipo Mulungu simunkamudziwa mʼdzikoli.+
12 Pa nthawi imene ija, Khristu simunkamudziwa, munali otalikirana ndi mtundu wa Isiraeli komanso simunali nawo mʼmapangano a lonjezo.+ Munalibe chiyembekezo ndipo Mulungu simunkamudziwa mʼdzikoli.+