1 Akorinto 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi inu simukudziwa kuti ndinu kachisi wa Mulungu+ ndipo mzimu wa Mulungu ukukhala mkati mwanu?+ 1 Akorinto 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi inu simukudziwa kuti thupi lanu ndi kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu, womwe munapatsidwa ndi Mulungu?+ Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+
19 Kodi inu simukudziwa kuti thupi lanu ndi kachisi+ wa mzimu woyera umene uli mwa inu, womwe munapatsidwa ndi Mulungu?+ Ndiponso mwiniwake wa inuyo si inu,+