28 Mulungu wapereka zochita kwa munthu aliyense mumpingo. Choyamba atumwi,+ chachiwiri aneneri,+ chachitatu aphunzitsi,+ kenako ntchito zamphamvu,+ mphatso zochiritsa,+ utumiki wothandiza anthu, luso loyendetsa zinthu+ ndiponso mphatso zolankhula zilankhulo zosiyanasiyana.+