Machitidwe 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri ndi aphunzitsi.+ Iwo anali Baranaba, Sumiyoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo wa ku Kurene, Saulo ndiponso Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo. Yakobo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Abale anga, pasakhale aphunzitsi ambiri pakati panu, podziwa kuti tidzalandira chiweruzo chokhwima.+
13 Mumpingo wa ku Antiokeya munali aneneri ndi aphunzitsi.+ Iwo anali Baranaba, Sumiyoni wotchedwa Nigeri, Lukiyo wa ku Kurene, Saulo ndiponso Manayeni amene anaphunzira pamodzi ndi Herode wolamulira chigawo.
3 Abale anga, pasakhale aphunzitsi ambiri pakati panu, podziwa kuti tidzalandira chiweruzo chokhwima.+