Machitidwe 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zitatero atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iwo anali osangalala+ chifukwa Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.
41 Zitatero atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iwo anali osangalala+ chifukwa Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.