Aroma 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Mulungu alibe tsankho.+ 1 Petulo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso ngati mukupempha zinthu kwa Atate, amene amaweruza mopanda tsankho+ mogwirizana ndi zimene aliyense amachita, muzichita zinthu zosonyeza kuti mumaopa Mulungu+ pamene mukukhala mʼdzikoli monga alendo.
17 Ndiponso ngati mukupempha zinthu kwa Atate, amene amaweruza mopanda tsankho+ mogwirizana ndi zimene aliyense amachita, muzichita zinthu zosonyeza kuti mumaopa Mulungu+ pamene mukukhala mʼdzikoli monga alendo.