15 Ndiye chifukwa chake inenso, kuyambira pamene ndinamva za chikhulupiriro chimene muli nacho mwa Ambuye Yesu komanso chikondi chimene mumachisonyeza kwa oyera onse, 16 sindinaleke kuyamika Mulungu chifukwa cha inu. Ndikupitirizabe kukupemphererani,