Aefeso 1:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu anaikanso zinthu zonse pansi pa mapazi ake,+ ndipo anamuika kuti akhale mutu wa zinthu zonse zimene ndi zokhudzana ndi mpingo+ 23 umene ndi thupi lake+ ndipo ndi wodzaza ndi Khristu, amene amadzaza zinthu zonse mokwanira.
22 Mulungu anaikanso zinthu zonse pansi pa mapazi ake,+ ndipo anamuika kuti akhale mutu wa zinthu zonse zimene ndi zokhudzana ndi mpingo+ 23 umene ndi thupi lake+ ndipo ndi wodzaza ndi Khristu, amene amadzaza zinthu zonse mokwanira.