9 Koma pamene ndinasowa zofunika zina ndili kwanuko, sindinalemetse munthu aliyense, popeza abale amene anachokera ku Makedoniya anandipatsa zonse zimene ndinkafunikira.+ Ndithu, ndinayesetsa kuti ndisakulemetseni mʼnjira iliyonse, ndipo ndipitirizabe kutero.+