-
1 Atesalonika 1:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Nthawi zonse timathokoza Mulungu tikamakutchulani nonsenu mʼmapemphero athu.+ 3 Timachita zimenezi chifukwa nthawi zonse timakumbukira ntchito zanu zachikhulupiriro, ntchito zanu zachikondi komanso kupirira kwanu chifukwa cha chiyembekezo chimene muli nacho+ mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, pamaso pa Mulungu amene ndi Atate wathu.
-