Luka 11:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Tsoka kwa inu odziwa Chilamulo, chifukwa munalanda anthu kiyi yowathandiza kudziwa zinthu. Inuyo simunalowemo,* ndipo anthu amene akufuna kulowamo mukuwatsekereza!”+ Machitidwe 13:49, 50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Komanso, mawu a Yehova* anapitiriza kufalitsidwa mʼdziko lonselo. 50 Koma Ayuda anauza zoipa amayi otchuka oopa Mulungu komanso amuna olemekezeka amumzindawo. Choncho iwo anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.
52 Tsoka kwa inu odziwa Chilamulo, chifukwa munalanda anthu kiyi yowathandiza kudziwa zinthu. Inuyo simunalowemo,* ndipo anthu amene akufuna kulowamo mukuwatsekereza!”+
49 Komanso, mawu a Yehova* anapitiriza kufalitsidwa mʼdziko lonselo. 50 Koma Ayuda anauza zoipa amayi otchuka oopa Mulungu komanso amuna olemekezeka amumzindawo. Choncho iwo anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.