-
Aroma 6:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndikulankhulatu ngati munthu chifukwa cha kufooka kwa matupi anu. Mmene munaperekera ziwalo zanu kuti zikhale akapolo a zonyansa ndiponso akapolo a kusamvera malamulo nʼcholinga chakuti muzichita zinthu zophwanya malamulo, perekaninso ziwalo zanu kuti mukhale akapolo a chilungamo ndiponso oyera.+
-