Aroma 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamabwezere choipa pa choipa.+ Muziganizira zimene anthu onse amaziona kuti ndi zabwino. Aroma 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Okondedwa, musamabwezere zoipa, koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Chifukwa Malemba amati: “‘Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine,’ watero Yehova.”*+
19 Okondedwa, musamabwezere zoipa, koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Chifukwa Malemba amati: “‘Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine,’ watero Yehova.”*+