Aroma 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiponso amene anawasankhiratu+ ndi amene anawaitana.+ Amene anawaitanawo ndi amenenso amawaona kuti ndi olungama.+ Ndipo amene amawaona kuti ndi olungamawo ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+
30 Ndiponso amene anawasankhiratu+ ndi amene anawaitana.+ Amene anawaitanawo ndi amenenso amawaona kuti ndi olungama.+ Ndipo amene amawaona kuti ndi olungamawo ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+