6 Kapena kodi ine ndekha ndi Baranaba+ ndi amene tilibe ufulu wosiya kugwira ntchito kuti tizipeza zofunika pa moyo? 7 Kodi alipo msilikali amene amatumikira, koma nʼkumadzilipira yekha? Ndani amalima munda wa mpesa koma osadya zipatso zake?+ Kapena ndani amaweta ziweto koma osamwa mkaka wake?