Aefeso 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu wakuba asiye kubako, koma azigwira ntchito molimbikira. Azigwira ntchito yabwino ndi manja ake+ kuti azitha kupeza zinthu zimene angathe kugawana ndi munthu wosowa.+
28 Munthu wakuba asiye kubako, koma azigwira ntchito molimbikira. Azigwira ntchito yabwino ndi manja ake+ kuti azitha kupeza zinthu zimene angathe kugawana ndi munthu wosowa.+