2 Atesalonika 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano abale tikukupatsani malangizo mʼdzina la Ambuye Yesu Khristu, kuti muzipewa mʼbale aliyense amene akuyenda mosalongosoka+ komanso amene akuchita zinthu zosagwirizana ndi malangizo amene* tinakupatsani.*+
6 Tsopano abale tikukupatsani malangizo mʼdzina la Ambuye Yesu Khristu, kuti muzipewa mʼbale aliyense amene akuyenda mosalongosoka+ komanso amene akuchita zinthu zosagwirizana ndi malangizo amene* tinakupatsani.*+