Levitiko 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musamabere anzanu mwachinyengo+ ndipo musamalande zinthu za aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone mʼnyumba mwanu mpaka mʼmawa.+ Mateyu 10:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musatenge golide, siliva kapena kopa* mʼzikwama zanu za ndalama.+ 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo kapena malaya awiri* kapena nsapato kapenanso ndodo+ chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+ Luka 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho muzikhala mʼnyumba imeneyo+ ndipo muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako nʼkupita kunyumba zina. Agalatiya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo agawane zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+
13 Musamabere anzanu mwachinyengo+ ndipo musamalande zinthu za aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone mʼnyumba mwanu mpaka mʼmawa.+
9 Musatenge golide, siliva kapena kopa* mʼzikwama zanu za ndalama.+ 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo kapena malaya awiri* kapena nsapato kapenanso ndodo+ chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+
7 Choncho muzikhala mʼnyumba imeneyo+ ndipo muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako nʼkupita kunyumba zina.
6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo agawane zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+