1 Akorinto 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho musaweruze+ chilichonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike. Iye adzachititsa kuti zinsinsi zamumdima zionekere komanso adzaonetsa poyera zimene zili mumtima. Ndiyeno aliyense payekha adzayamikiridwa ndi Mulungu.+
5 Choncho musaweruze+ chilichonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike. Iye adzachititsa kuti zinsinsi zamumdima zionekere komanso adzaonetsa poyera zimene zili mumtima. Ndiyeno aliyense payekha adzayamikiridwa ndi Mulungu.+