-
Agalatiya 1:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Koma pamene Mulungu, amene anandichititsa kuti ndibadwe komanso kundiitana kudzera mu kukoma mtima kwake kwakukulu,+ anaona kuti nʼzabwino kuti 16 aulule za Mwana wake kudzera mwa ine, nʼcholinga choti ndilengeze kwa anthu a mitundu ina+ uthenga wabwino wonena za iye, sindinapite kukakambirana ndi munthu aliyense* nthawi yomweyo.
-