1 Timoteyo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akulu amene amatsogolera bwino+ azilemekezedwa kwambiri,+ makamaka amene amachita khama polankhula Mawu a Mulungu ndiponso kuphunzitsa.+ 2 Timoteyo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu. Koma ayenera kukhala wodekha kwa onse,+ woyenerera kuphunzitsa, wougwira mtima ena akamulakwira+ Tito 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Popeza ndi mtumiki* wa Mulungu, woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera. Asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa, wankhanza* kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo. Tito 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akhalenso wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi mfundo zolondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.
17 Akulu amene amatsogolera bwino+ azilemekezedwa kwambiri,+ makamaka amene amachita khama polankhula Mawu a Mulungu ndiponso kuphunzitsa.+
24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu. Koma ayenera kukhala wodekha kwa onse,+ woyenerera kuphunzitsa, wougwira mtima ena akamulakwira+
7 Popeza ndi mtumiki* wa Mulungu, woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera. Asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa, wankhanza* kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo.
9 Akhalenso wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi mfundo zolondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.