23 Koma mukuyenera kupitiriza kukhala mogwirizana ndi chikhulupiriro chanu,+ muli okhazikika pamaziko,+ muli olimba+ komanso muli osasunthika pa chiyembekezo cha uthenga wabwino umene munamva, umenenso unalalikidwa padziko lonse.+ Ineyo Paulo ndinakhala mtumiki wa uthenga wabwino umenewu.+