1 Akorinto 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 ndipo amakhala wogawanika. Nayenso mkazi wosakwatiwa komanso namwali, amadera nkhawa zinthu za Ambuye,+ kuti akhale woyera mʼthupi lake ndi maganizo ake.* Koma mkazi wokwatiwa amadera nkhawa zinthu zamʼdziko, mmene angakondweretsere mwamuna wake.
34 ndipo amakhala wogawanika. Nayenso mkazi wosakwatiwa komanso namwali, amadera nkhawa zinthu za Ambuye,+ kuti akhale woyera mʼthupi lake ndi maganizo ake.* Koma mkazi wokwatiwa amadera nkhawa zinthu zamʼdziko, mmene angakondweretsere mwamuna wake.