2 Akorinto 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tikakumana ndi mayesero,* inuyo mumatonthozedwa ndiponso kupulumutsidwa. Tikatonthozedwa, nanunso mumatonthozedwa ndipo zimenezi zimathandiza kuti mupirire mavuto amene nafenso tikukumana nawo. Aefeso 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndikukupemphani kuti musafooke poona mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, popeza mavuto amene ndikukumana nawowa achititsa kuti mulandire ulemerero.+ Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+
6 Tikakumana ndi mayesero,* inuyo mumatonthozedwa ndiponso kupulumutsidwa. Tikatonthozedwa, nanunso mumatonthozedwa ndipo zimenezi zimathandiza kuti mupirire mavuto amene nafenso tikukumana nawo.
13 Choncho ndikukupemphani kuti musafooke poona mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, popeza mavuto amene ndikukumana nawowa achititsa kuti mulandire ulemerero.+
24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+