Machitidwe 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ayuda amene anabwera kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala nʼkumukokera kunja kwa mzindawo poganiza kuti wafa.+
19 Ndiyeno Ayuda amene anabwera kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala nʼkumukokera kunja kwa mzindawo poganiza kuti wafa.+