16 Kenako Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wa Chiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki. 2 Abale a ku Lusitara ndi ku Ikoniyo anapereka umboni wabwino wonena za iyeyo.