1 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe mawu ouziridwa amanena momveka bwino kuti nthawi ina mʼtsogolo, chikhulupiriro cha anthu ena chidzatha chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso zinthu zimene ziwanda zimaphunzitsa.
4 Komabe mawu ouziridwa amanena momveka bwino kuti nthawi ina mʼtsogolo, chikhulupiriro cha anthu ena chidzatha chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso zinthu zimene ziwanda zimaphunzitsa.