Machitidwe 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo ndiye anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo mʼkachisi.
29 Iwo ananena zimenezi chifukwa tsiku lina anaona Terofimo+ wa ku Efeso ali naye limodzi mumzindawo ndiye anaganiza kuti Paulo analowetsa Terofimo mʼkachisi.