Aroma 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+
17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+