Aroma 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano ndikukulimbikitsani abale, kuti musamale ndi amene amagawanitsa anthu ndiponso kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi zimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+ 2 Yohane 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wina akabwera ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire mʼnyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.
17 Tsopano ndikukulimbikitsani abale, kuti musamale ndi amene amagawanitsa anthu ndiponso kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi zimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+
10 Wina akabwera ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire mʼnyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.