-
Numeri 18:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ine ndatenga Alevi omwe ndi abale anu pakati pa Aisiraeli ndipo ndawapereka kwa inu kuti akhale mphatso yanu.+ Iwo aperekedwa kwa Yehova kuti azitumikira pachihema chokumanako.+ 7 Iweyo ndi ana ako, udindo wanu ndi kugwira ntchito zaunsembe paguwa lansembe komanso pa zinthu zamkati ndi kuseri kwa katani.+ Umenewu ndi utumiki wanu.+ Ndakupatsani utumiki waunsembe kuti ukhale mphatso kwa inu, ndipo munthu wamba* aliyense akayandikira pafupi aziphedwa.”+
-