Luka 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikuimira pangano latsopano+ limene linakhazikitsidwa pogwiritsa ntchito magazi anga,+ amene adzakhetsedwe chifukwa cha inu.+ 1 Timoteyo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa pali Mulungu mmodzi+ ndiponso mkhalapakati mmodzi+ pakati pa Mulungu ndi anthu.+ Mkhalapakatiyu ndi Khristu Yesu,+ munthu Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,* Aheberi 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi amene awazidwa, omwe amalankhula mʼnjira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+
20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikuimira pangano latsopano+ limene linakhazikitsidwa pogwiritsa ntchito magazi anga,+ amene adzakhetsedwe chifukwa cha inu.+
5 Chifukwa pali Mulungu mmodzi+ ndiponso mkhalapakati mmodzi+ pakati pa Mulungu ndi anthu.+ Mkhalapakatiyu ndi Khristu Yesu,+ munthu
22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,*
24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi amene awazidwa, omwe amalankhula mʼnjira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+