8 Pa zimene tikunenazi, mfundo yaikulu ndi yakuti: Tili ndi mkulu wa ansembe ngati ameneyu,+ ndipo iye wakhala kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka kumwamba.+ 2 Iye ndi mtumiki wamʼmalo oyerawo+ komanso mʼchihema chenicheni, chomangidwa ndi Yehova osati munthu.