2 Akorinto 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Popeza Mulungu ndi amene anati: “Kuwale kuchokera mumdima,”+ ndipo pogwiritsa ntchito nkhope ya Khristu waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudza kudziwa Mulungu. Aheberi 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analandirapo mphatso yaulere yakumwamba, amene analandira mzimu woyera
6 Popeza Mulungu ndi amene anati: “Kuwale kuchokera mumdima,”+ ndipo pogwiritsa ntchito nkhope ya Khristu waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudza kudziwa Mulungu.
4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analandirapo mphatso yaulere yakumwamba, amene analandira mzimu woyera