Mateyu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho aliyense amene akuvomereza pamaso pa anthu kuti ndi wophunzira wanga,+ inenso ndidzamuvomereza pamaso pa Atate wanga wakumwamba kuti ndi wophunzira wanga.+ 1 Akorinto 15:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba+ ndiponso osasunthika. Nthawi zonse muzikhala ndi zochita zambiri+ pa ntchito ya Ambuye, podziwa kuti zonse zimene mukuchita pa ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+
32 Choncho aliyense amene akuvomereza pamaso pa anthu kuti ndi wophunzira wanga,+ inenso ndidzamuvomereza pamaso pa Atate wanga wakumwamba kuti ndi wophunzira wanga.+
58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba+ ndiponso osasunthika. Nthawi zonse muzikhala ndi zochita zambiri+ pa ntchito ya Ambuye, podziwa kuti zonse zimene mukuchita pa ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+