Genesis 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbadwa* zako ngati nyenyezi zakumwamba komanso ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.+ Ndipo mbadwa yako idzalanda mzinda* wa adani ake.+ 1 Mafumu 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ayuda ndi Aisiraeli anachuluka kwambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja+ ndipo ankadya, kumwa komanso kusangalala.+
17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbadwa* zako ngati nyenyezi zakumwamba komanso ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.+ Ndipo mbadwa yako idzalanda mzinda* wa adani ake.+
20 Ayuda ndi Aisiraeli anachuluka kwambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja+ ndipo ankadya, kumwa komanso kusangalala.+