16 Kudzera mwa iye, Mulungu analenga zinthu zina zonse kumwamba ndi padziko lapansi. Analenga zinthu zooneka ndi zinthu zosaoneka,+ kaya ndi mipando yachifumu, ambuye, maboma komanso maulamuliro. Inde, analenga zinthu zina zonse kudzera mwa iye+ ndiponso chifukwa cha iye.