Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+
18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+