Yohane 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu anamuuza kuti: “Usandikangamire chifukwa nthawi yoti ndipite kwa Atate sinakwane. Koma pita kwa abale anga+ ndipo ukawauze kuti, ‘Ine ndikupita kwa Atate wanga+ ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”
17 Yesu anamuuza kuti: “Usandikangamire chifukwa nthawi yoti ndipite kwa Atate sinakwane. Koma pita kwa abale anga+ ndipo ukawauze kuti, ‘Ine ndikupita kwa Atate wanga+ ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”