20 Popeza chilengedwe chinaweruzidwa kuti chikhale chopanda pake,+ osati mwa kufuna kwake koma kudzera mwa amene anachiweruza. Ndipo anaperekanso chiyembekezo 21 chakuti chilengedwecho chidzamasulidwa+ ku ukapolo wa thupi limene limawonongeka nʼkukhala ndi ufulu waulemerero wa ana a Mulungu.