Afilipi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikuyesetsa kuti ndikwaniritse cholinga changa chokalandira mphoto.+ Mphoto imeneyi ndi kukakhala ndi moyo kumwamba+ ndipo Mulungu adzaipereka kwa anthu amene anawaitana kudzera mwa Khristu Yesu. 1 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tinkachita zimenezi nʼcholinga choti mupitirize kuyenda mʼnjira imene Mulungu amafuna.+ Iye ndi amene akukuitanani kuti mulowe mu Ufumu wake+ ndi kulandira ulemerero.+
14 Ndikuyesetsa kuti ndikwaniritse cholinga changa chokalandira mphoto.+ Mphoto imeneyi ndi kukakhala ndi moyo kumwamba+ ndipo Mulungu adzaipereka kwa anthu amene anawaitana kudzera mwa Khristu Yesu.
12 Tinkachita zimenezi nʼcholinga choti mupitirize kuyenda mʼnjira imene Mulungu amafuna.+ Iye ndi amene akukuitanani kuti mulowe mu Ufumu wake+ ndi kulandira ulemerero.+