-
Genesis 2:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Pofika tsiku la 7, Mulungu anali atamaliza ntchito imene ankagwira. Pa tsiku la 7 limeneli, iye anayamba kupuma pa ntchito yonse imene ankagwira.+ 3 Kenako Mulungu anadalitsa tsiku la 7 komanso ananena kuti likhale lopatulika, chifukwa kuyambira pa tsikuli wakhala akupuma pa ntchito yake yonse. Pamenepa Mulungu anali atamaliza kulenga zinthu zonse zimene ankafuna.
-