Mateyu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Siyani kuweruza ena+ kuti inunso musaweruzidwe, Luka 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Komanso, siyani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Siyani kutsutsa ena ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+ Aroma 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa+ chifukwa Yehova* akhoza kumuthandiza kuti zimuyendere bwino.
37 Komanso, siyani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Siyani kutsutsa ena ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+
4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa+ chifukwa Yehova* akhoza kumuthandiza kuti zimuyendere bwino.