Luka 12:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndiyeno kapolo ameneyo, amene anadziwa zimene mbuye wake ankafuna koma osakonzekera kubwera kwake kapena kuchita zimene anamuuza,* adzakwapulidwa zikoti zambiri.+ Yohane 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yesu anawauza kuti: “Mukanakhala osaona, simukanakhala ndi tchimo. Koma popeza mukunena kuti ‘Tikuona,’ tchimo lanu silidzakhululukidwa.”+ Yohane 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndikanapanda kubwera kudzalankhula nawo, akanakhala opanda tchimo.+ Koma tsopano sangakane tchimo lawo.+
47 Ndiyeno kapolo ameneyo, amene anadziwa zimene mbuye wake ankafuna koma osakonzekera kubwera kwake kapena kuchita zimene anamuuza,* adzakwapulidwa zikoti zambiri.+
41 Yesu anawauza kuti: “Mukanakhala osaona, simukanakhala ndi tchimo. Koma popeza mukunena kuti ‘Tikuona,’ tchimo lanu silidzakhululukidwa.”+
22 Ndikanapanda kubwera kudzalankhula nawo, akanakhala opanda tchimo.+ Koma tsopano sangakane tchimo lawo.+