Miyambo 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu amene amadalira chuma chake adzakumana ndi mavuto,+Koma anthu olungama adzasangalala ngati mtengo wa masamba obiriwira.+ Luka 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma tsoka kwa inu amene muli achuma,+ chifukwa mukulandiriratu zonse zokusangalatsani.+ Luka 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunena zoona, nʼzosavuta kuti ngamila ilowe pakabowo ka singano kusiyana nʼkuti munthu wolemera alowe mu Ufumu wa Mulungu.”+
28 Munthu amene amadalira chuma chake adzakumana ndi mavuto,+Koma anthu olungama adzasangalala ngati mtengo wa masamba obiriwira.+
25 Kunena zoona, nʼzosavuta kuti ngamila ilowe pakabowo ka singano kusiyana nʼkuti munthu wolemera alowe mu Ufumu wa Mulungu.”+