Akolose 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma tsopano muyenera kutaya zonsezo kutali ndi inu. Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa+ komanso mawu achipongwe+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+ 1 Petulo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho siyani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka komanso miseche yamtundu uliwonse.
8 Koma tsopano muyenera kutaya zonsezo kutali ndi inu. Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa+ komanso mawu achipongwe+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+
2 Choncho siyani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka komanso miseche yamtundu uliwonse.