29 Ndiyeno Mlevi, amene sanapatsidwe gawo kapena cholowa ngati inuyo, komanso mlendo, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye amene akukhala mumzinda wanu, azibwera kudzadya ndi kukhuta+ kuti Yehova Mulungu wanu akudalitseni pa chilichonse chimene mukuchita.”+