1 Mafumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mundipatse ine mtumiki wanu mtima womvera kuti ndiweruze anthu anu+ komanso ndizitha kusiyanitsa zabwino ndi zoipa.+ Ndani angathe kuweruza anthu anu ambirimbiriwa?”* Maliko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, zinthu zonse zimene mukupempha ndi kuzipempherera, muzikhulupirira kuti mwazilandira kale ndipo mudzazilandiradi.+ 1 Yohane 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo chilichonse chimene tingamupemphe adzatipatsa,+ chifukwa timamvera malamulo ake komanso tikuchita zinthu zomusangalatsa.
9 Mundipatse ine mtumiki wanu mtima womvera kuti ndiweruze anthu anu+ komanso ndizitha kusiyanitsa zabwino ndi zoipa.+ Ndani angathe kuweruza anthu anu ambirimbiriwa?”*
24 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, zinthu zonse zimene mukupempha ndi kuzipempherera, muzikhulupirira kuti mwazilandira kale ndipo mudzazilandiradi.+
22 Ndipo chilichonse chimene tingamupemphe adzatipatsa,+ chifukwa timamvera malamulo ake komanso tikuchita zinthu zomusangalatsa.