Chivumbulutso 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso kuti pali anthu amene amanena kuti ndi Ayuda ndipo amakunyoza. Koma sikuti iwo ndi Ayuda, mʼmalomwake iwo ndi sunagoge wa Satana.+
9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso kuti pali anthu amene amanena kuti ndi Ayuda ndipo amakunyoza. Koma sikuti iwo ndi Ayuda, mʼmalomwake iwo ndi sunagoge wa Satana.+